Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 98 - الأعرَاف - Page - Juz 9
﴿أَوَأَمِنَ أَهۡلُ ٱلۡقُرَىٰٓ أَن يَأۡتِيَهُم بَأۡسُنَا ضُحٗى وَهُمۡ يَلۡعَبُونَ ﴾
[الأعرَاف: 98]
﴿أو أمن أهل القرى أن يأتيهم بأسنا ضحى وهم يلعبون﴾ [الأعرَاف: 98]
Khaled Ibrahim Betala “Kapena anthu a m’mizindayo ali ndi chitetezo cholimba kuti chilango Chathu sichingawafike masana uku iwo akusewera |