Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma‘arij ayat 1 - المَعَارج - Page - Juz 29
﴿سَأَلَ سَآئِلُۢ بِعَذَابٖ وَاقِعٖ ﴾
[المَعَارج: 1]
﴿سأل سائل بعذاب واقع﴾ [المَعَارج: 1]
Khaled Ibrahim Betala “Wopempha adapempha kuti chiwadzere msanga chilango chopezekacho, (m’kupempha kwa chipongwe ndi kotsutsa) |