Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jinn ayat 17 - الجِن - Page - Juz 29
﴿لِّنَفۡتِنَهُمۡ فِيهِۚ وَمَن يُعۡرِضۡ عَن ذِكۡرِ رَبِّهِۦ يَسۡلُكۡهُ عَذَابٗا صَعَدٗا ﴾
[الجِن: 17]
﴿لنفتنهم فيه ومن يعرض عن ذكر ربه يسلكه عذابا صعدا﴾ [الجِن: 17]
Khaled Ibrahim Betala “Kuti tiwayese ndi zimenezo (mmene angamyamikire Allah pa mtendere Wake pa iwo). Koma amene anyozera kupembedza Mbuye wake, amlowetsa ku chilango chovuta (chimene sangathe kupirira nacho) |