Quran with Chichewa translation - Surah Al-Muzzammil ayat 14 - المُزمل - Page - Juz 29
﴿يَوۡمَ تَرۡجُفُ ٱلۡأَرۡضُ وَٱلۡجِبَالُ وَكَانَتِ ٱلۡجِبَالُ كَثِيبٗا مَّهِيلًا ﴾
[المُزمل: 14]
﴿يوم ترجف الأرض والجبال وكانت الجبال كثيبا مهيلا﴾ [المُزمل: 14]
Khaled Ibrahim Betala “Tsiku limene nthaka ndi mapiri zidzagwedezeka; (kugwedezeka kwa mphamvu kotero kuti) mapiri adzakhala ngati mulu wa mchenga woyoyoka |