×

Matambula oonetsa zinthu zomwe zili m’kati mwake, opangidwa kuchokera ku siliva. Iwo 76:16 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Insan ⮕ (76:16) ayat 16 in Chichewa

76:16 Surah Al-Insan ayat 16 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Insan ayat 16 - الإنسَان - Page - Juz 29

﴿قَوَارِيرَاْ مِن فِضَّةٖ قَدَّرُوهَا تَقۡدِيرٗا ﴾
[الإنسَان: 16]

Matambula oonetsa zinthu zomwe zili m’kati mwake, opangidwa kuchokera ku siliva. Iwo adzathiramo chakumwa molingana ndi chilakolako chawo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قواريرا من فضة قدروها تقديرا, باللغة نيانجا

﴿قواريرا من فضة قدروها تقديرا﴾ [الإنسَان: 16]

Khaled Ibrahim Betala
“Zolangala zopangidwa ku siliva, atalinga bwino zakumwazo (malinga ndi kufuna kwawo)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek