Quran with Chichewa translation - Surah Al-Insan ayat 15 - الإنسَان - Page - Juz 29
﴿وَيُطَافُ عَلَيۡهِم بِـَٔانِيَةٖ مِّن فِضَّةٖ وَأَكۡوَابٖ كَانَتۡ قَوَارِيرَا۠ ﴾
[الإنسَان: 15]
﴿ويطاف عليهم بآنية من فضة وأكواب كانت قواريرا﴾ [الإنسَان: 15]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo adzakhala akuzunguliridwa (ndi otumikira) uku atatenga zomwera za siliva ndi matambula onyezimira ndiponso olangala |