Quran with Chichewa translation - Surah Al-Insan ayat 17 - الإنسَان - Page - Juz 29
﴿وَيُسۡقَوۡنَ فِيهَا كَأۡسٗا كَانَ مِزَاجُهَا زَنجَبِيلًا ﴾
[الإنسَان: 17]
﴿ويسقون فيها كأسا كان مزاجها زنجبيلا﴾ [الإنسَان: 17]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo (anthu abwino) akamwetsedwa kumeneko vinyo, chosakanizira chake chikafanana ndi Zanjabila (chikasu) |