Quran with Chichewa translation - Surah Al-Insan ayat 4 - الإنسَان - Page - Juz 29
﴿إِنَّآ أَعۡتَدۡنَا لِلۡكَٰفِرِينَ سَلَٰسِلَاْ وَأَغۡلَٰلٗا وَسَعِيرًا ﴾
[الإنسَان: 4]
﴿إنا أعتدنا للكافرين سلاسل وأغلالا وسعيرا﴾ [الإنسَان: 4]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu Ife okana tawakonzera unyolo (wam’miyendo yawo) ndi magoli (am’manja ndi m’makosi awo) ndi Moto waukali woyaka |