Quran with Chichewa translation - Surah An-Nazi‘at ayat 12 - النَّازعَات - Page - Juz 30
﴿قَالُواْ تِلۡكَ إِذٗا كَرَّةٌ خَاسِرَةٞ ﴾
[النَّازعَات: 12]
﴿قالوا تلك إذا كرة خاسرة﴾ [النَّازعَات: 12]
Khaled Ibrahim Betala “Adanena (mokanira ndi mwachipongwe): “Choncho kubwerera kumeneko ngati kudzakhalepodi kudzakhala kotaika (ndi kopanda phindu kwa ife. Pomwe ife sindife oyenera kutaika).” |