Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 22 - الأنفَال - Page - Juz 9
﴿۞ إِنَّ شَرَّ ٱلدَّوَآبِّ عِندَ ٱللَّهِ ٱلصُّمُّ ٱلۡبُكۡمُ ٱلَّذِينَ لَا يَعۡقِلُونَ ﴾
[الأنفَال: 22]
﴿إن شر الدواب عند الله الصم البكم الذين لا يعقلون﴾ [الأنفَال: 22]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu nyama zoipitsitsa pamaso pa Allah ndi agonthi, abubu amene alibe nzeru, (omwe ndi aphatikizi ndi anthu achinyengo) |