Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 21 - الأنفَال - Page - Juz 9
﴿وَلَا تَكُونُواْ كَٱلَّذِينَ قَالُواْ سَمِعۡنَا وَهُمۡ لَا يَسۡمَعُونَ ﴾
[الأنفَال: 21]
﴿ولا تكونوا كالذين قالوا سمعنا وهم لا يسمعون﴾ [الأنفَال: 21]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo musakhale monga aja achinyengo omwe akunena: “Tamva (choonadi ndipo tachisunga),” pomwe iwo sakumva (kumva kochigonjera) |