×

Oh inu anthu okhulupirira! Ngati inu mumvera ndi kuopa Mulungu, Iye adzakupatsani 8:29 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:29) ayat 29 in Chichewa

8:29 Surah Al-Anfal ayat 29 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 29 - الأنفَال - Page - Juz 9

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُوٓاْ إِن تَتَّقُواْ ٱللَّهَ يَجۡعَل لَّكُمۡ فُرۡقَانٗا وَيُكَفِّرۡ عَنكُمۡ سَيِّـَٔاتِكُمۡ وَيَغۡفِرۡ لَكُمۡۗ وَٱللَّهُ ذُو ٱلۡفَضۡلِ ٱلۡعَظِيمِ ﴾
[الأنفَال: 29]

Oh inu anthu okhulupirira! Ngati inu mumvera ndi kuopa Mulungu, Iye adzakupatsani nzeru zodziwira chabwino ndi choipa ndipo adzakukhululukirani machimo anu ndipo Mulungu ndiye Mwini chuma chochuluka

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها الذين آمنوا إن تتقوا الله يجعل لكم فرقانا ويكفر عنكم سيئاتكم, باللغة نيانجا

﴿ياأيها الذين آمنوا إن تتقوا الله يجعل لكم فرقانا ويكفر عنكم سيئاتكم﴾ [الأنفَال: 29]

Khaled Ibrahim Betala
“E inu amene mwakhulupirira! Ngati muopa Allah, adzakupatsani chilekanitso (cholekanitsa pakati pa choonadi ndi chachabe), ndiponso akufafanizirani zoipa zanu ndi kukukhululukirani. Ndipo Allah ndi Mwini ubwino waukulu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek