×

Iwe ukadawaona angelo pamene amachotsa mizimu ya anthu osakhulupirira! Iwo amamenya pa 8:50 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:50) ayat 50 in Chichewa

8:50 Surah Al-Anfal ayat 50 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 50 - الأنفَال - Page - Juz 10

﴿وَلَوۡ تَرَىٰٓ إِذۡ يَتَوَفَّى ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ ٱلۡمَلَٰٓئِكَةُ يَضۡرِبُونَ وُجُوهَهُمۡ وَأَدۡبَٰرَهُمۡ وَذُوقُواْ عَذَابَ ٱلۡحَرِيقِ ﴾
[الأنفَال: 50]

Iwe ukadawaona angelo pamene amachotsa mizimu ya anthu osakhulupirira! Iwo amamenya pa nkhope ndi pa misana yawo nati: “Lawani ululu wa moto wa ku Gahena.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولو ترى إذ يتوفى الذين كفروا الملائكة يضربون وجوههم وأدبارهم وذوقوا عذاب, باللغة نيانجا

﴿ولو ترى إذ يتوفى الذين كفروا الملائكة يضربون وجوههم وأدبارهم وذوقوا عذاب﴾ [الأنفَال: 50]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ukadaona angelo pamene akuchotsa miyoyo ya anthu amene sadakhulupirire (pa imfa yawo) uku akumenya kunkhope zawo ndi kumisana yawo (uku akunena): “Lawani chilango cha Moto woocha. (Ukadaziona zoopsa kwabasi).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek