×

Pamene anthu a chinyengo pamodzi ndi anthu amene m’mitima mwawo mudali matenda 8:49 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:49) ayat 49 in Chichewa

8:49 Surah Al-Anfal ayat 49 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 49 - الأنفَال - Page - Juz 10

﴿إِذۡ يَقُولُ ٱلۡمُنَٰفِقُونَ وَٱلَّذِينَ فِي قُلُوبِهِم مَّرَضٌ غَرَّ هَٰٓؤُلَآءِ دِينُهُمۡۗ وَمَن يَتَوَكَّلۡ عَلَى ٱللَّهِ فَإِنَّ ٱللَّهَ عَزِيزٌ حَكِيمٞ ﴾
[الأنفَال: 49]

Pamene anthu a chinyengo pamodzi ndi anthu amene m’mitima mwawo mudali matenda adati: “Anthu awa ali kunyengedwa ndi chipembedzo chawo.” Koma aliyense amene aika chikhulupiriro chake mwa Mulungu, ndithudi, Mulungu ndi Wamphamvu ndi Wanzeru

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إذ يقول المنافقون والذين في قلوبهم مرض غر هؤلاء دينهم ومن يتوكل, باللغة نيانجا

﴿إذ يقول المنافقون والذين في قلوبهم مرض غر هؤلاء دينهم ومن يتوكل﴾ [الأنفَال: 49]

Khaled Ibrahim Betala
“(Kumbukirani) pamene achiphamaso ndi amene ali ndi matenda m’mitima mwawo amanena: “Anthu awa chipembedzo chawo (cha Chisilamu) chawanyenga.” Komatu amene akuyadzamira kwa Allah ndithudi Allah Ngwamphamvu zoposa, Ngwanzeru zakuya
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek