Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 59 - الأنفَال - Page - Juz 10
﴿وَلَا يَحۡسَبَنَّ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ سَبَقُوٓاْۚ إِنَّهُمۡ لَا يُعۡجِزُونَ ﴾
[الأنفَال: 59]
﴿ولا يحسبن الذين كفروا سبقوا إنهم لا يعجزون﴾ [الأنفَال: 59]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo (anthu) amene sadakhulupirire asaganize kuti ampitilira (Allah kotero kuti sachita kanthu ndi iwo), iwo sangamulepheretse Allah (chimene akufuna kuchita pa iwo) |