×

Ngati iwe uopa chinyengo chochokera kwa anthu, nawenso abwezere mwawubwino machitidwe omwewo. 8:58 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:58) ayat 58 in Chichewa

8:58 Surah Al-Anfal ayat 58 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 58 - الأنفَال - Page - Juz 10

﴿وَإِمَّا تَخَافَنَّ مِن قَوۡمٍ خِيَانَةٗ فَٱنۢبِذۡ إِلَيۡهِمۡ عَلَىٰ سَوَآءٍۚ إِنَّ ٱللَّهَ لَا يُحِبُّ ٱلۡخَآئِنِينَ ﴾
[الأنفَال: 58]

Ngati iwe uopa chinyengo chochokera kwa anthu, nawenso abwezere mwawubwino machitidwe omwewo. Ndithudi Mulungu sakonda anthu aupandu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإما تخافن من قوم خيانة فانبذ إليهم على سواء إن الله لا, باللغة نيانجا

﴿وإما تخافن من قوم خيانة فانبذ إليهم على سواء إن الله لا﴾ [الأنفَال: 58]

Khaled Ibrahim Betala
“Ngati uopa kusakhulupirika kwa anthu (omwe unapangana nawo chipangano), atayire (chipangano chawocho), mwachilungamo; ndithu Allah sakonda (anthu) osakhulupirika
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek