×

Ndipo ngati iwo afuna kukunyenga ndithudi Mulungu ndi wokwanira kwa iwe. Iye 8:62 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:62) ayat 62 in Chichewa

8:62 Surah Al-Anfal ayat 62 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 62 - الأنفَال - Page - Juz 10

﴿وَإِن يُرِيدُوٓاْ أَن يَخۡدَعُوكَ فَإِنَّ حَسۡبَكَ ٱللَّهُۚ هُوَ ٱلَّذِيٓ أَيَّدَكَ بِنَصۡرِهِۦ وَبِٱلۡمُؤۡمِنِينَ ﴾
[الأنفَال: 62]

Ndipo ngati iwo afuna kukunyenga ndithudi Mulungu ndi wokwanira kwa iwe. Iye ndiye amene adakulimbikitsa pokupatsa chithandizo chake ndi anthu okhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإن يريدوا أن يخدعوك فإن حسبك الله هو الذي أيدك بنصره وبالمؤمنين, باللغة نيانجا

﴿وإن يريدوا أن يخدعوك فإن حسبك الله هو الذي أيدك بنصره وبالمؤمنين﴾ [الأنفَال: 62]

Khaled Ibrahim Betala
“Ngati afuna kukunyenga pa chimvanochi, ndithudi, Allah akukwanira kwa iwe (kukuteteza). Iye ndi Yemwe anakuthangata ndi chipulumutso chake ndi okhulupirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek