×

Ndipo Iye wayanjanitsa mitima yawo. Ngati iwe ukadawononga zinthu zonse za padziko 8:63 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:63) ayat 63 in Chichewa

8:63 Surah Al-Anfal ayat 63 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 63 - الأنفَال - Page - Juz 10

﴿وَأَلَّفَ بَيۡنَ قُلُوبِهِمۡۚ لَوۡ أَنفَقۡتَ مَا فِي ٱلۡأَرۡضِ جَمِيعٗا مَّآ أَلَّفۡتَ بَيۡنَ قُلُوبِهِمۡ وَلَٰكِنَّ ٱللَّهَ أَلَّفَ بَيۡنَهُمۡۚ إِنَّهُۥ عَزِيزٌ حَكِيمٞ ﴾
[الأنفَال: 63]

Ndipo Iye wayanjanitsa mitima yawo. Ngati iwe ukadawononga zinthu zonse za padziko lapansi iwe siukadatha kuyanjanitsa mitima yawo ayi koma Mulungu waiyanjanitsa. Ndithudi Iye ndi Wamphamvu ndi Wanzeru

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وألف بين قلوبهم لو أنفقت ما في الأرض جميعا ما ألفت بين, باللغة نيانجا

﴿وألف بين قلوبهم لو أنفقت ما في الأرض جميعا ما ألفت بين﴾ [الأنفَال: 63]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (Allah) analuzanitsa pakati pa mitima yawo (poika chikondi pakati pawo). Ngati ukanapereka zonse za m’dziko lapansi (ncholinga choti uwaluzanitse mitima yawo mwa iwe wekha) sukadatha kuluzanitsa pakati pa mitima yawo. Koma Allah adaluzanitsa pakati pawo. Ndithu Iye Ngwamphamvu zoposa Ngwanzeru zakuya
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek