×

Ndipo iwo amene adakhulupirira pambuyo pake kale ndipo adasamuka ndi kumenya nkhondo 8:75 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:75) ayat 75 in Chichewa

8:75 Surah Al-Anfal ayat 75 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 75 - الأنفَال - Page - Juz 10

﴿وَٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ مِنۢ بَعۡدُ وَهَاجَرُواْ وَجَٰهَدُواْ مَعَكُمۡ فَأُوْلَٰٓئِكَ مِنكُمۡۚ وَأُوْلُواْ ٱلۡأَرۡحَامِ بَعۡضُهُمۡ أَوۡلَىٰ بِبَعۡضٖ فِي كِتَٰبِ ٱللَّهِۚ إِنَّ ٱللَّهَ بِكُلِّ شَيۡءٍ عَلِيمُۢ ﴾
[الأنفَال: 75]

Ndipo iwo amene adakhulupirira pambuyo pake kale ndipo adasamuka ndi kumenya nkhondo pamodzi ndi iwe, iwo ndi abale ako. Koma ubale wa magazi amodzi umakhala woganiziridwa polandira katundu malinga ndi malamulo a Mulungu amene adaperekedwa. Ndithudi Mulungu amadziwa zinthu zonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذين آمنوا من بعد وهاجروا وجاهدوا معكم فأولئك منكم وأولو الأرحام بعضهم, باللغة نيانجا

﴿والذين آمنوا من بعد وهاجروا وجاهدوا معكم فأولئك منكم وأولو الأرحام بعضهم﴾ [الأنفَال: 75]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo aja akhulupirira pambuyo (pa Amuhajirina ndi Answari), nawonso nasamukira (ku Madina kukakhala pamodzi ndi Mtumiki ndi Asilamu anzawo), namenyanso nkhondo pamodzi nanu, iwo ndi amene ali mwa inu. Koma achibale chakubadwana, ndiamene ali oyenera (kulowerana mmalo pa chuma) ena ndi ena, mmene zilili) m’buku la Allah. Ndithudi, Allah Ngodziwa chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek