Quran with Chichewa translation - Surah ‘Abasa ayat 23 - عَبَسَ - Page - Juz 30
﴿كـَلَّا لَمَّا يَقۡضِ مَآ أَمَرَهُۥ ﴾
[عَبَسَ: 23]
﴿كلا لما يقض ما أمره﴾ [عَبَسَ: 23]
Khaled Ibrahim Betala “Ayi ndithu (munthu) sanakwaniritsebe zimene adamulamula Mbuye wake (Allah chingakhale wakhala nthawi yaitali pa dziko lapansi) |