Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 100 - التوبَة - Page - Juz 11
﴿وَٱلسَّٰبِقُونَ ٱلۡأَوَّلُونَ مِنَ ٱلۡمُهَٰجِرِينَ وَٱلۡأَنصَارِ وَٱلَّذِينَ ٱتَّبَعُوهُم بِإِحۡسَٰنٖ رَّضِيَ ٱللَّهُ عَنۡهُمۡ وَرَضُواْ عَنۡهُ وَأَعَدَّ لَهُمۡ جَنَّٰتٖ تَجۡرِي تَحۡتَهَا ٱلۡأَنۡهَٰرُ خَٰلِدِينَ فِيهَآ أَبَدٗاۚ ذَٰلِكَ ٱلۡفَوۡزُ ٱلۡعَظِيمُ ﴾
[التوبَة: 100]
﴿والسابقون الأولون من المهاجرين والأنصار والذين اتبعوهم بإحسان رضي الله عنهم ورضوا﴾ [التوبَة: 100]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo amene adatsogolera poyamba, a m’gulu la Amuhajirina ndi Answari, ndi omwe adawatsatira iwo mwa ubwino, Allah adzakondwa nawo. Naonso adzakondwera Naye (pa zomwe adzapatsidwa ndi Allah). Ndipo wawakonzera minda yomwe mitsinje ikuyenda pansi (ndi pasogolo) pake, adzakhala m’menemo muyaya. Uko ndikupambana kwakukulu |