Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 108 - التوبَة - Page - Juz 11
﴿لَا تَقُمۡ فِيهِ أَبَدٗاۚ لَّمَسۡجِدٌ أُسِّسَ عَلَى ٱلتَّقۡوَىٰ مِنۡ أَوَّلِ يَوۡمٍ أَحَقُّ أَن تَقُومَ فِيهِۚ فِيهِ رِجَالٞ يُحِبُّونَ أَن يَتَطَهَّرُواْۚ وَٱللَّهُ يُحِبُّ ٱلۡمُطَّهِّرِينَ ﴾
[التوبَة: 108]
﴿لا تقم فيه أبدا لمسجد أسس على التقوى من أول يوم أحق﴾ [التوبَة: 108]
Khaled Ibrahim Betala “Usaimilire (ndi kupemphera) m’menemo mpang’ono pomwe. Ndithu msikiti umene udakhazikitsidwa poyamba ncholinga choopa Allah ndiwo wofunika kuti uimilire m’menemo (ndi kupemphera). M’menemo muli anthu okonda kudziyeretsa (matupi ndi mitima yawo); ndipo Allah amakonda odziyeretsa |