×

Kotero yendani mwa ufulu miyezi inayi m’dziko lonse. Koma muyenera kudziwa kuti 9:2 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:2) ayat 2 in Chichewa

9:2 Surah At-Taubah ayat 2 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 2 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿فَسِيحُواْ فِي ٱلۡأَرۡضِ أَرۡبَعَةَ أَشۡهُرٖ وَٱعۡلَمُوٓاْ أَنَّكُمۡ غَيۡرُ مُعۡجِزِي ٱللَّهِ وَأَنَّ ٱللَّهَ مُخۡزِي ٱلۡكَٰفِرِينَ ﴾
[التوبَة: 2]

Kotero yendani mwa ufulu miyezi inayi m’dziko lonse. Koma muyenera kudziwa kuti inu simungathawe Mulungu ndipo Mulungu adzachititsa manyazi anthu osakhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فسيحوا في الأرض أربعة أشهر واعلموا أنكم غير معجزي الله وأن الله, باللغة نيانجا

﴿فسيحوا في الأرض أربعة أشهر واعلموا أنكم غير معجزي الله وأن الله﴾ [التوبَة: 2]

Khaled Ibrahim Betala
“(Auze Amushirikina kuti): Yendani pa dziko miyezi inayi basi. (Pambuyo pake sipadzakhala chitetezo pakati pawo ndi ife). Ndipo dziwani kuti inu simungathe kumpambana Allah. Ndipo Allah Ngosambula osakhulupirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek