×

Ndithudi iwo adakonza chiwembu chokuukira ndipo anasokoneza chili chonse mpaka pamene chilungamo 9:48 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:48) ayat 48 in Chichewa

9:48 Surah At-Taubah ayat 48 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 48 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿لَقَدِ ٱبۡتَغَوُاْ ٱلۡفِتۡنَةَ مِن قَبۡلُ وَقَلَّبُواْ لَكَ ٱلۡأُمُورَ حَتَّىٰ جَآءَ ٱلۡحَقُّ وَظَهَرَ أَمۡرُ ٱللَّهِ وَهُمۡ كَٰرِهُونَ ﴾
[التوبَة: 48]

Ndithudi iwo adakonza chiwembu chokuukira ndipo anasokoneza chili chonse mpaka pamene chilungamo chinadza ndipo ulamuliro wa Mulungu unakhazikika angakhale iwo anali kudana nawo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لقد ابتغوا الفتنة من قبل وقلبوا لك الأمور حتى جاء الحق وظهر, باللغة نيانجا

﴿لقد ابتغوا الفتنة من قبل وقلبوا لك الأمور حتى جاء الحق وظهر﴾ [التوبَة: 48]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithudi, akhala akukufunirani chisokonezo kuyambira kale, akusanthulirasanthulira zinthu (n’cholinga choti athane nawe) kufikira choonadi chadza ndi kuonekera poyera lamulo la Allah (lowakhaulitsa Ayuda) iwo asakufuna
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek