Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 49 - التوبَة - Page - Juz 10
﴿وَمِنۡهُم مَّن يَقُولُ ٱئۡذَن لِّي وَلَا تَفۡتِنِّيٓۚ أَلَا فِي ٱلۡفِتۡنَةِ سَقَطُواْۗ وَإِنَّ جَهَنَّمَ لَمُحِيطَةُۢ بِٱلۡكَٰفِرِينَ ﴾
[التوبَة: 49]
﴿ومنهم من يقول ائذن لي ولا تفتني ألا في الفتنة سقطوا وإن﴾ [التوبَة: 49]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo mwa iwo pali yemwe akuti: “Ndiloreni ine (kuti nditsale ku nkhondo) ndipo musandiponye m’mayeso (kuopa kuti ndingalakwe ndikaona akazi akumeneko).” Dziwani kuti iwo agwera kale m’mayesero. Ndipo, ndithu Jahannam ikawazinga mbali zonse osakhulupirira |