×

Nena, “Perekani mwachifuniro chanu kapena mokakamizidwa, koma palibe chimene chidzalandiridwa kuchokera kwa 9:53 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:53) ayat 53 in Chichewa

9:53 Surah At-Taubah ayat 53 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 53 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿قُلۡ أَنفِقُواْ طَوۡعًا أَوۡ كَرۡهٗا لَّن يُتَقَبَّلَ مِنكُمۡ إِنَّكُمۡ كُنتُمۡ قَوۡمٗا فَٰسِقِينَ ﴾
[التوبَة: 53]

Nena, “Perekani mwachifuniro chanu kapena mokakamizidwa, koma palibe chimene chidzalandiridwa kuchokera kwa inu. Ndithudi inu ndinu anthu ochita zoipa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل أنفقوا طوعا أو كرها لن يتقبل منكم إنكم كنتم قوما فاسقين, باللغة نيانجا

﴿قل أنفقوا طوعا أو كرها لن يتقبل منكم إنكم كنتم قوما فاسقين﴾ [التوبَة: 53]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena (kwa achiphamaso): “Perekani (chuma chanu) mwa chifuniro kapena mosafuna sichizalandiridwa kwa inu. Ndithu inu ndinu anthu otuluka m’chilamulo cha Allah.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek