Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 6 - التوبَة - Page - Juz 10
﴿وَإِنۡ أَحَدٞ مِّنَ ٱلۡمُشۡرِكِينَ ٱسۡتَجَارَكَ فَأَجِرۡهُ حَتَّىٰ يَسۡمَعَ كَلَٰمَ ٱللَّهِ ثُمَّ أَبۡلِغۡهُ مَأۡمَنَهُۥۚ ذَٰلِكَ بِأَنَّهُمۡ قَوۡمٞ لَّا يَعۡلَمُونَ ﴾
[التوبَة: 6]
﴿وإن أحد من المشركين استجارك فأجره حتى يسمع كلام الله ثم أبلغه﴾ [التوبَة: 6]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ngati mmodzi wa Amushirikina Atakupempha chitetezo (kuti amvere mawu a Allah), mtetezeni kuti amve mawu a Allah. Kenako (ngati sadakhutitsidwe nawo), mpititseni kumalo kwake mwamtendere (ngati safuna kulowa m’Chisilamu). Izi nchifukwa chakuti iwo ndi anthu osadziwa |