×

Ngati uwafunsa, iwo amati: “Ife timangocheza ndi kusewera basi.” Nena: “Kodi ndi 9:65 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:65) ayat 65 in Chichewa

9:65 Surah At-Taubah ayat 65 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 65 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿وَلَئِن سَأَلۡتَهُمۡ لَيَقُولُنَّ إِنَّمَا كُنَّا نَخُوضُ وَنَلۡعَبُۚ قُلۡ أَبِٱللَّهِ وَءَايَٰتِهِۦ وَرَسُولِهِۦ كُنتُمۡ تَسۡتَهۡزِءُونَ ﴾
[التوبَة: 65]

Ngati uwafunsa, iwo amati: “Ife timangocheza ndi kusewera basi.” Nena: “Kodi ndi Mulungu, chivumbulutso chake ndi Mtumwi wake amene munali kunyoza?”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولئن سألتهم ليقولن إنما كنا نخوض ونلعب قل أبالله وآياته ورسوله كنتم, باللغة نيانجا

﴿ولئن سألتهم ليقولن إنما كنا نخوض ونلعب قل أبالله وآياته ورسوله كنتم﴾ [التوبَة: 65]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo utawafunsa (chifukwa ninji chipembedzo akuchichitira chipongwe)? Anena: “Ife timangosereula ndi kusewera basi (palibe china).” Nena: “Mumachitira Allah ndi Ayah (ndime) Zake ndi Mtumiki Wake zachipongwe?”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek