Quran with Chichewa translation - Surah Al-Balad ayat 4 - البَلَد - Page - Juz 30
﴿لَقَدۡ خَلَقۡنَا ٱلۡإِنسَٰنَ فِي كَبَدٍ ﴾
[البَلَد: 4]
﴿لقد خلقنا الإنسان في كبد﴾ [البَلَد: 4]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithudi tamulenga munthu mmavuto (kuyambira chiyambi chake mpaka malekezero a moyo wake) |