Quran with Chichewa translation - Surah Yunus ayat 44 - يُونس - Page - Juz 11
﴿إِنَّ ٱللَّهَ لَا يَظۡلِمُ ٱلنَّاسَ شَيۡـٔٗا وَلَٰكِنَّ ٱلنَّاسَ أَنفُسَهُمۡ يَظۡلِمُونَ ﴾
[يُونس: 44]
﴿إن الله لا يظلم الناس شيئا ولكن الناس أنفسهم يظلمون﴾ [يُونس: 44]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu Allah sachitira anthu choipa chilichonse. Koma anthu akudzichitira okha zoipa. (Adapatsidwa nzeru, koma sazigwiritsa ntchito) |