Quran with Chichewa translation - Surah Yunus ayat 67 - يُونس - Page - Juz 11
﴿هُوَ ٱلَّذِي جَعَلَ لَكُمُ ٱلَّيۡلَ لِتَسۡكُنُواْ فِيهِ وَٱلنَّهَارَ مُبۡصِرًاۚ إِنَّ فِي ذَٰلِكَ لَأٓيَٰتٖ لِّقَوۡمٖ يَسۡمَعُونَ ﴾
[يُونس: 67]
﴿هو الذي جعل لكم الليل لتسكنوا فيه والنهار مبصرا إن في ذلك﴾ [يُونس: 67]
Khaled Ibrahim Betala “Iye (Allah) ndi Yemwe adakupangirani usiku kuti muzipumamo, ndi (adakupangirani) usana kukhala wowala (kuti mupenye). Ndithu m’zimene muli zisonyezo (zosonyeza chifundo cha Allah pa zolengedwa Zake) kwa anthu akumva |