Quran with Chichewa translation - Surah Hud ayat 80 - هُود - Page - Juz 12
﴿قَالَ لَوۡ أَنَّ لِي بِكُمۡ قُوَّةً أَوۡ ءَاوِيٓ إِلَىٰ رُكۡنٖ شَدِيدٖ ﴾
[هُود: 80]
﴿قال لو أن لي بكم قوة أو آوي إلى ركن شديد﴾ [هُود: 80]
Khaled Ibrahim Betala “(Iye) adati: “Ndikadakhala nayo mphamvu (yomenyana nanu) kapena kotsamira kolimba kwamphamvu (ndikadalimbana nanu kuti musachite zauve ndi alendowa).” |