Quran with Chichewa translation - Surah Hud ayat 79 - هُود - Page - Juz 12
﴿قَالُواْ لَقَدۡ عَلِمۡتَ مَا لَنَا فِي بَنَاتِكَ مِنۡ حَقّٖ وَإِنَّكَ لَتَعۡلَمُ مَا نُرِيدُ ﴾
[هُود: 79]
﴿قالوا لقد علمت ما لنا في بناتك من حق وإنك لتعلم ما﴾ [هُود: 79]
Khaled Ibrahim Betala “(Iwo) adati: “Ndithu ukudziwa bwino kuti tilibe khumbo ndi atsikana ako. Ndipo ndithu iwe ukudziwa bwino chimene tifuna.” |