×

Mpaka pamene Atumwi athu adataya mtima ndipo anali kuganiza kuti kulibe wina 12:110 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:110) ayat 110 in Chichewa

12:110 Surah Yusuf ayat 110 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 110 - يُوسُف - Page - Juz 13

﴿حَتَّىٰٓ إِذَا ٱسۡتَيۡـَٔسَ ٱلرُّسُلُ وَظَنُّوٓاْ أَنَّهُمۡ قَدۡ كُذِبُواْ جَآءَهُمۡ نَصۡرُنَا فَنُجِّيَ مَن نَّشَآءُۖ وَلَا يُرَدُّ بَأۡسُنَا عَنِ ٱلۡقَوۡمِ ٱلۡمُجۡرِمِينَ ﴾
[يُوسُف: 110]

Mpaka pamene Atumwi athu adataya mtima ndipo anali kuganiza kuti kulibe wina aliyense amene akadawakhulupirira iwo, thandizo lathu lidadza pa iwo ndi kupulumutsa aliyense amene Ife tidamufuna. Ndipo chilango chathu sichingabweretsedwe m’mbuyo kwa anthu ochita zoipa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: حتى إذا استيأس الرسل وظنوا أنهم قد كذبوا جاءهم نصرنا فنجي من, باللغة نيانجا

﴿حتى إذا استيأس الرسل وظنوا أنهم قد كذبوا جاءهم نصرنا فنجي من﴾ [يُوسُف: 110]

Khaled Ibrahim Betala
“Mpaka pamene atumiki adataya mtima (za anthu awo) nkuganiza kuti ayesedwa onama, chithandizo chathu chidawadzera, ndipo amene tidawafuna adapulumuka. Koma chilango chathu sichibwezedwa kwa anthu oipa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek