×

Ndithudi m’mbiri yawo muli phunziro kwa anthu ozindikira. Iyi si nkhani yopeka 12:111 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:111) ayat 111 in Chichewa

12:111 Surah Yusuf ayat 111 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 111 - يُوسُف - Page - Juz 13

﴿لَقَدۡ كَانَ فِي قَصَصِهِمۡ عِبۡرَةٞ لِّأُوْلِي ٱلۡأَلۡبَٰبِۗ مَا كَانَ حَدِيثٗا يُفۡتَرَىٰ وَلَٰكِن تَصۡدِيقَ ٱلَّذِي بَيۡنَ يَدَيۡهِ وَتَفۡصِيلَ كُلِّ شَيۡءٖ وَهُدٗى وَرَحۡمَةٗ لِّقَوۡمٖ يُؤۡمِنُونَ ﴾
[يُوسُف: 111]

Ndithudi m’mbiri yawo muli phunziro kwa anthu ozindikira. Iyi si nkhani yopeka ayi koma ndi chitsimikiziro cha ma buku a Mulungu amene adaperekedwa kale, ndipo ndi mfotokozi wa zinthu zonse ndi chilangizo ndiponso madalitso kwa anthu okhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لقد كان في قصصهم عبرة لأولي الألباب ما كان حديثا يفترى ولكن, باللغة نيانجا

﴿لقد كان في قصصهم عبرة لأولي الألباب ما كان حديثا يفترى ولكن﴾ [يُوسُف: 111]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu m’nkhani zawo izi muli phunziro kwa eni nzeru. (Qur’aniyi) simawu opekedwa, koma (iyi Qur’an) ndi chitsimikizo cha zomwe zidalipo patsogolo pake (m’mabuku ena a Allah), ndi kumasulira kwa tsatanetsatane pa chilichonse ndiponso chiongoko ndi mtendere kwa anthu okhulupirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek