×

Yosefe adati,“ohAmbuye wanga! Ndende ndi yabwino kwa ine kuposa zimene akundiitanira. Ngati 12:33 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:33) ayat 33 in Chichewa

12:33 Surah Yusuf ayat 33 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 33 - يُوسُف - Page - Juz 12

﴿قَالَ رَبِّ ٱلسِّجۡنُ أَحَبُّ إِلَيَّ مِمَّا يَدۡعُونَنِيٓ إِلَيۡهِۖ وَإِلَّا تَصۡرِفۡ عَنِّي كَيۡدَهُنَّ أَصۡبُ إِلَيۡهِنَّ وَأَكُن مِّنَ ٱلۡجَٰهِلِينَ ﴾
[يُوسُف: 33]

Yosefe adati,“ohAmbuye wanga! Ndende ndi yabwino kwa ine kuposa zimene akundiitanira. Ngati inu simunditchinjiriza kuchiwembu chawo ine ndidzapendekera kwa iwo ndikukhala mmodzi wa anthu osadziwa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال رب السجن أحب إلي مما يدعونني إليه وإلا تصرف عني كيدهن, باللغة نيانجا

﴿قال رب السجن أحب إلي مما يدعونني إليه وإلا تصرف عني كيدهن﴾ [يُوسُف: 33]

Khaled Ibrahim Betala
“(Yûsuf) adati: “E Mbuye wanga! Ndende ndi yabwino kwa ine kuposa izi akundiitanira. Ngati simundichotsera ndale zawo ndiye kuti ndiwacheukira ndikukhala mmodzi mwa mbuli.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek