Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 35 - يُوسُف - Page - Juz 12
﴿ثُمَّ بَدَا لَهُم مِّنۢ بَعۡدِ مَا رَأَوُاْ ٱلۡأٓيَٰتِ لَيَسۡجُنُنَّهُۥ حَتَّىٰ حِينٖ ﴾
[يُوسُف: 35]
﴿ثم بدا لهم من بعد ما رأوا الآيات ليسجننه حتى حين﴾ [يُوسُف: 35]
Khaled Ibrahim Betala “Kenako kudaoneka kwa iwo, (nduna ndi anthu ake) pambuyo poona zizindikiro (zonse zakuyeretsedwa kwa Yûsuf) kuti akamponye kundende kwa nthawi yochepa (pofuna kumusungira ulemu mkazi wa nduna) |