Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 36 - يُوسُف - Page - Juz 12
﴿وَدَخَلَ مَعَهُ ٱلسِّجۡنَ فَتَيَانِۖ قَالَ أَحَدُهُمَآ إِنِّيٓ أَرَىٰنِيٓ أَعۡصِرُ خَمۡرٗاۖ وَقَالَ ٱلۡأٓخَرُ إِنِّيٓ أَرَىٰنِيٓ أَحۡمِلُ فَوۡقَ رَأۡسِي خُبۡزٗا تَأۡكُلُ ٱلطَّيۡرُ مِنۡهُۖ نَبِّئۡنَا بِتَأۡوِيلِهِۦٓۖ إِنَّا نَرَىٰكَ مِنَ ٱلۡمُحۡسِنِينَ ﴾
[يُوسُف: 36]
﴿ودخل معه السجن فتيان قال أحدهما إني أراني أعصر خمرا وقال الآخر﴾ [يُوسُف: 36]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo anyamata awiri adalowa m’ndende pamodzi ndi iye. Mmodzi mwa iwo adati (kumuuza Yûsuf): “Ndithu ine ndalota ndikufulula mowa.” Ndipo wina adati: “Ndithu ine ndalota ndikusenza mikate pamutu panga yomwe idali kudyedwa ndi mbalame. Tiuze tanthauzo lake. Ndithu ife tikukuona iwe kuti ndiwe mmodzi wa anthu abwino.” |