×

“Ndipo potha izi kudzadza zaka zisanu ndi ziwiri za chilala pamene mudzadya 12:48 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:48) ayat 48 in Chichewa

12:48 Surah Yusuf ayat 48 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 48 - يُوسُف - Page - Juz 12

﴿ثُمَّ يَأۡتِي مِنۢ بَعۡدِ ذَٰلِكَ سَبۡعٞ شِدَادٞ يَأۡكُلۡنَ مَا قَدَّمۡتُمۡ لَهُنَّ إِلَّا قَلِيلٗا مِّمَّا تُحۡصِنُونَ ﴾
[يُوسُف: 48]

“Ndipo potha izi kudzadza zaka zisanu ndi ziwiri za chilala pamene mudzadya zimene mudasunga kupatula pang’ono zimene mudzasunge.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ثم يأتي من بعد ذلك سبع شداد يأكلن ما قدمتم لهن إلا, باللغة نيانجا

﴿ثم يأتي من بعد ذلك سبع شداد يأكلن ما قدمتم لهن إلا﴾ [يُوسُف: 48]

Khaled Ibrahim Betala
““Kenako pambuyo pake zidzadza zaka zisanu ndi ziwiri za masautso zomwe zidzadya zimene mudasunga m’mbuyo, kupatula zochepa zimene muzidzazisunga (mobisa kuti zidzakhale mbewu.)”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek