×

Yosefe adati, “Inu mudzabzala zaka zisanu ndi ziwiri monga momwe mumachitira ndipo 12:47 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:47) ayat 47 in Chichewa

12:47 Surah Yusuf ayat 47 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 47 - يُوسُف - Page - Juz 12

﴿قَالَ تَزۡرَعُونَ سَبۡعَ سِنِينَ دَأَبٗا فَمَا حَصَدتُّمۡ فَذَرُوهُ فِي سُنۢبُلِهِۦٓ إِلَّا قَلِيلٗا مِّمَّا تَأۡكُلُونَ ﴾
[يُوسُف: 47]

Yosefe adati, “Inu mudzabzala zaka zisanu ndi ziwiri monga momwe mumachitira ndipo zimene muzikolola muzizisiya mumakoko ake kupatula pang’ono zomwe muzidya.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال تزرعون سبع سنين دأبا فما حصدتم فذروه في سنبله إلا قليلا, باللغة نيانجا

﴿قال تزرعون سبع سنين دأبا فما حصدتم فذروه في سنبله إلا قليلا﴾ [يُوسُف: 47]

Khaled Ibrahim Betala
“(Yûsuf) adati: “Mudzalima zaka zisanu ndi ziwiri mondondozana ndi mwakhama ndipo zimene mwakolola zisiyeni m’ngala zake, kupatula zochepa zimene muzidzadya (kuti zam’ngalazo mudzadye mzaka zanjala).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek