×

“Koma ngati inu simudzabwera naye kwa ine inu simudzalandira muyeso wa chakudya 12:60 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:60) ayat 60 in Chichewa

12:60 Surah Yusuf ayat 60 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 60 - يُوسُف - Page - Juz 13

﴿فَإِن لَّمۡ تَأۡتُونِي بِهِۦ فَلَا كَيۡلَ لَكُمۡ عِندِي وَلَا تَقۡرَبُونِ ﴾
[يُوسُف: 60]

“Koma ngati inu simudzabwera naye kwa ine inu simudzalandira muyeso wa chakudya kuchokera kwa ine ndiponso simudzandiyandikira.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فإن لم تأتوني به فلا كيل لكم عندي ولا تقربون, باللغة نيانجا

﴿فإن لم تأتوني به فلا كيل لكم عندي ولا تقربون﴾ [يُوسُف: 60]

Khaled Ibrahim Betala
““Koma ngati simudzandibweretsera iye, simudzakhala ndi mulingo (wachakudya) kwa ine, ndipo musadzandiyandikire.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek