×

Iwo adzalowa ku Paradiso kwa muyaya pamodzi ndi ena a makolo awo 13:23 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ar-Ra‘d ⮕ (13:23) ayat 23 in Chichewa

13:23 Surah Ar-Ra‘d ayat 23 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Ra‘d ayat 23 - الرَّعد - Page - Juz 13

﴿جَنَّٰتُ عَدۡنٖ يَدۡخُلُونَهَا وَمَن صَلَحَ مِنۡ ءَابَآئِهِمۡ وَأَزۡوَٰجِهِمۡ وَذُرِّيَّٰتِهِمۡۖ وَٱلۡمَلَٰٓئِكَةُ يَدۡخُلُونَ عَلَيۡهِم مِّن كُلِّ بَابٖ ﴾
[الرَّعد: 23]

Iwo adzalowa ku Paradiso kwa muyaya pamodzi ndi ena a makolo awo angwiro, ndi akazi awo ndi ana awo. Kuchokera ku khomo lililonse angelo adzadza nati kwa iwo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: جنات عدن يدخلونها ومن صلح من آبائهم وأزواجهم وذرياتهم والملائكة يدخلون عليهم, باللغة نيانجا

﴿جنات عدن يدخلونها ومن صلح من آبائهم وأزواجهم وذرياتهم والملائكة يدخلون عليهم﴾ [الرَّعد: 23]

Khaled Ibrahim Betala
“Minda yamuyaya adzailowa iwo (pamodzi) ndi amene adachita zabwino mwa makolo awo, akazi awo ndi ana awo; ndipo angelo azikalowa kwa iwo khomo lililonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek