Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Ra‘d ayat 24 - الرَّعد - Page - Juz 13
﴿سَلَٰمٌ عَلَيۡكُم بِمَا صَبَرۡتُمۡۚ فَنِعۡمَ عُقۡبَى ٱلدَّارِ ﴾
[الرَّعد: 24]
﴿سلام عليكم بما صبرتم فنعم عقبى الدار﴾ [الرَّعد: 24]
Khaled Ibrahim Betala “(Uku akunena): “Salaamun Alayikumu (Mtendere uli pa inu) chifukwa chakupirira kwanu (pochita zabwino ndi kusiya zoipa ndi kukhala mwaubwino ndi anzanu)! Taona kukhala bwino zotsatira za Nyumba ya tsiku la chimaliziro.” |