×

Ndi iwo amene amapirira chifukwa chofuna mtendere wa Mulungu modzipereka, amapitiriza mapemphero 13:22 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ar-Ra‘d ⮕ (13:22) ayat 22 in Chichewa

13:22 Surah Ar-Ra‘d ayat 22 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Ra‘d ayat 22 - الرَّعد - Page - Juz 13

﴿وَٱلَّذِينَ صَبَرُواْ ٱبۡتِغَآءَ وَجۡهِ رَبِّهِمۡ وَأَقَامُواْ ٱلصَّلَوٰةَ وَأَنفَقُواْ مِمَّا رَزَقۡنَٰهُمۡ سِرّٗا وَعَلَانِيَةٗ وَيَدۡرَءُونَ بِٱلۡحَسَنَةِ ٱلسَّيِّئَةَ أُوْلَٰٓئِكَ لَهُمۡ عُقۡبَى ٱلدَّارِ ﴾
[الرَّعد: 22]

Ndi iwo amene amapirira chifukwa chofuna mtendere wa Mulungu modzipereka, amapitiriza mapemphero awo ndi kupereka zimene tawapatsa mseri kapena moonekera, ndipo amaletsa choipa pochita chinthu chabwino. Awa ndiwo amene adzaone zinthu zokoma

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذين صبروا ابتغاء وجه ربهم وأقاموا الصلاة وأنفقوا مما رزقناهم سرا وعلانية, باللغة نيانجا

﴿والذين صبروا ابتغاء وجه ربهم وأقاموا الصلاة وأنفقوا مما رزقناهم سرا وعلانية﴾ [الرَّعد: 22]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndi omwenso amapirira chifukwa chofuna chiyanjo cha Mbuye wawo ndi kupemphera Swala ndi kupereka mu zomwe tawapatsa, mobisa ndi moonekera, ndi kuchotsa choipa ndi chabwino (pochita chabwino pa choipacho); iwo ndi omwe adzapeza malipiro (abwino) a ku Nyumba ya tsiku la chimaliziro
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek