Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Ra‘d ayat 39 - الرَّعد - Page - Juz 13
﴿يَمۡحُواْ ٱللَّهُ مَا يَشَآءُ وَيُثۡبِتُۖ وَعِندَهُۥٓ أُمُّ ٱلۡكِتَٰبِ ﴾
[الرَّعد: 39]
﴿يمحوا الله ما يشاء ويثبت وعنده أم الكتاب﴾ [الرَّعد: 39]
Khaled Ibrahim Betala “Allah amafafaniza zimene wafuna ndi kulimbikitsa (kuti zisachoke zomwe wafuna), ndipo gwero la malamulo onse lili kwa Iye (Allah) |