Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Ra‘d ayat 40 - الرَّعد - Page - Juz 13
﴿وَإِن مَّا نُرِيَنَّكَ بَعۡضَ ٱلَّذِي نَعِدُهُمۡ أَوۡ نَتَوَفَّيَنَّكَ فَإِنَّمَا عَلَيۡكَ ٱلۡبَلَٰغُ وَعَلَيۡنَا ٱلۡحِسَابُ ﴾
[الرَّعد: 40]
﴿وإن ما نرينك بعض الذي نعدهم أو نتوفينك فإنما عليك البلاغ وعلينا﴾ [الرَّعد: 40]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ngati tikusonyeza zina mwa (zilango) zimene tawalonjeza, kapena kukupatsa imfa (usanazione zilangozo, ndithu ziwafikabe). Ndithu udindo wako ndi kufikitsa uthenga basi (umene walamulidwa kuufikitsa kwa iwo) ndipo Ife udindo wathu ndi kuwerengera (zochita zawo) |