×

Kodi iwo saona mmene Ife timachepetsera malire a dziko pang’onopang’ono? Ndipo Mulungu 13:41 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ar-Ra‘d ⮕ (13:41) ayat 41 in Chichewa

13:41 Surah Ar-Ra‘d ayat 41 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Ra‘d ayat 41 - الرَّعد - Page - Juz 13

﴿أَوَلَمۡ يَرَوۡاْ أَنَّا نَأۡتِي ٱلۡأَرۡضَ نَنقُصُهَا مِنۡ أَطۡرَافِهَاۚ وَٱللَّهُ يَحۡكُمُ لَا مُعَقِّبَ لِحُكۡمِهِۦۚ وَهُوَ سَرِيعُ ٱلۡحِسَابِ ﴾
[الرَّعد: 41]

Kodi iwo saona mmene Ife timachepetsera malire a dziko pang’onopang’ono? Ndipo Mulungu akalamulira chinthu, palibe amene angatsutse. Iye ndi wachangu powerengera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أو لم يروا أنا نأتي الأرض ننقصها من أطرافها والله يحكم لا, باللغة نيانجا

﴿أو لم يروا أنا نأتي الأرض ننقصها من أطرافها والله يحكم لا﴾ [الرَّعد: 41]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi sadaone kuti tikulidzera dziko lawo ndi kulichepetserachepetsera malire ake? Ndipo Allah amalamula (mwachilungamo) palibe wotsutsa lamulo Lake. Ndipo Iye Ngwachangu pakuwerengera
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek