×

“Ndipo, ndithudi, tidzakukhazikitsani m’dziko pambuyo pa iwo. Chimenechi ndi cha iye amene 14:14 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ibrahim ⮕ (14:14) ayat 14 in Chichewa

14:14 Surah Ibrahim ayat 14 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ibrahim ayat 14 - إبراهِيم - Page - Juz 13

﴿وَلَنُسۡكِنَنَّكُمُ ٱلۡأَرۡضَ مِنۢ بَعۡدِهِمۡۚ ذَٰلِكَ لِمَنۡ خَافَ مَقَامِي وَخَافَ وَعِيدِ ﴾
[إبراهِيم: 14]

“Ndipo, ndithudi, tidzakukhazikitsani m’dziko pambuyo pa iwo. Chimenechi ndi cha iye amene aopa kudzaima pamaso panga ndipo amaopa chenjezo langa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولنسكننكم الأرض من بعدهم ذلك لمن خاف مقامي وخاف وعيد, باللغة نيانجا

﴿ولنسكننكم الأرض من بعدهم ذلك لمن خاف مقامي وخاف وعيد﴾ [إبراهِيم: 14]

Khaled Ibrahim Betala
““Ndipo tikukhazikani (inu) pambuyo pawo m’dzikomo. Apeza zimenezi omwe aopa kuimilira pamaso pa Ine, ndi kuopa chilango Chnga.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek