Quran with Chichewa translation - Surah Ibrahim ayat 13 - إبراهِيم - Page - Juz 13
﴿وَقَالَ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ لِرُسُلِهِمۡ لَنُخۡرِجَنَّكُم مِّنۡ أَرۡضِنَآ أَوۡ لَتَعُودُنَّ فِي مِلَّتِنَاۖ فَأَوۡحَىٰٓ إِلَيۡهِمۡ رَبُّهُمۡ لَنُهۡلِكَنَّ ٱلظَّٰلِمِينَ ﴾
[إبراهِيم: 13]
﴿وقال الذين كفروا لرسلهم لنخرجنكم من أرضنا أو لتعودن في ملتنا فأوحى﴾ [إبراهِيم: 13]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo amene sadakhulupirire, adanena kwa atumiki awo: “Ndithu tikutulutsani m’dziko lathu, pokhapokha mubwelere m’chipembedzo chathu.” Koma Mbuye wawo (Allah) adawavumbulutsira uthenga (wakuti): “Ndithu tiwaononga ochita zoipa (osakhulupirira).” |