Quran with Chichewa translation - Surah Ibrahim ayat 17 - إبراهِيم - Page - Juz 13
﴿يَتَجَرَّعُهُۥ وَلَا يَكَادُ يُسِيغُهُۥ وَيَأۡتِيهِ ٱلۡمَوۡتُ مِن كُلِّ مَكَانٖ وَمَا هُوَ بِمَيِّتٖۖ وَمِن وَرَآئِهِۦ عَذَابٌ غَلِيظٞ ﴾
[إبراهِيم: 17]
﴿يتجرعه ولا يكاد يسيغه ويأتيه الموت من كل مكان وما هو بميت﴾ [إبراهِيم: 17]
Khaled Ibrahim Betala “Adzakhala akumwa koma movutikira ndipo ululu wa imfa udzamdzera mbali zonse koma sadzafa; ndipo kuonjezera apo, pali chilango (china) chaukali |